Zomwe wayankhula Bon Kalindo Lero pa 13 July 2024 pa nkhani ya kutuluka kwa UTM mu Tonse Alliance

27,116
0
Published 2024-07-12

All Comments (21)
  • @GiftJacob-z4c
    Koma fact ndiyakut apapa a UTM mwaphunziladi angakhale achedwa koma this is brave idea , tili ku mbuyo kwanu .
  • @MphaKampala
    Uyuyu a Malawi ambr mmamupeputsa ,.koma nthw idzakwana ubwino wake muzaudziwa Chitsime chimaoneka chokuya madzi akaphwa
  • @MillieMalakam
    From town centre Mitchell's capetown bon ndimakudyadilan kwambili God ahead u bro
  • @SebenzileMsebe
    Utm bwelenani ku dpp kuti udzamange amene anapha chilima
  • @Eli-u2d
    Ndale zokha zokha,mwasiya masewero abwino, ndalama iwonongesa mbiri
  • Kalindo salimoyesa 🎉🎉🎉🎉🎉🎉👍👍👍👍💯
  • @user-yq1mc3nm1f
    Kkkkkk Manganya adali Yudasi zoona, bwato satsilana pakati pa nyanja kkkkkk
  • Nkhani ikhale UTM , AFORD ndi UDF apange alliance, president achoke ku UTM ndekuti azapeza ma vote Ku north , central pang'ono koma ochuluka ku southern nde kuti azaiphula bho bho
  • @MarkTembo-ut9sv
    Ku dpp tikataniko? Chilima anatulukako ndipo sanabwelere mpaka kufa kwake ndiye ife tufuna mufuna mzimu wake utikanthe?
  • @RuthChilobwe
    UTM ISAPHATIKIZANE NDI DPP CHIFUKWA MKAZI WA LOTI ANAYANG'ANA MBUYO POTHAWA MOTO KU SODOMU..PAMENE NGELO WA AMBUYE ANAWAUZA KUTI ALIYENSE ASAYANG'ANE MBUYO. KOMA MKAZI WAKE WA LOTI ANAYANG'ANA MBUYO POGANIZIRA MOWA WAKE WOMWE ANKAPHIKA KUSOMUKO NKUMAGULITSA. IYEO ANASANDUKA CHULU CHA MCHERE. SO UTM NSO MUKAPHATIKANA NDI DPP MUSANDUKA CHULU CHA MCHERE.MUKHALA STUCK AND DORMANT DEAD WOOD .!!!
  • @PemphoSmart
    Propaganda at its peak. Ife anthu osauka takana kuti ndiwe president wathu
  • @daudinussah2232
    Ubwino wake ovota ndife, and kalikonse kochitika pansi pathambo Mulungu amachionetsa poyera